Ekisodo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja. Salimo 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu.
8 Ndi mpweya wotuluka m’mphuno mwanu,+ madzi anaunjikika pamodzi.Madzi oyenda anaima ngati khoma.Madzi amphamvu anaundana pakatikati pa nyanja.
7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu.