2 Samueli 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo ngalande za pansi pa nyanja zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi+ anakhala poonekera,Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwa Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwake.+ Salimo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ngalande za pansi pa madzi zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi anakhala poonekera.+Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwanu.+
16 Ndipo ngalande za pansi pa nyanja zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi+ anakhala poonekera,Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwa Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwake.+
15 Ndipo ngalande za pansi pa madzi zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi anakhala poonekera.+Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwanu.+