Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+

  • Salimo 66:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Anasandutsa nyanja kukhala malo ouma,+

      Anthu anawoloka mtsinje mwa kuyenda ndi mapazi awo.+

      Pamenepo tinayamba kusangalala mwa iye.+

  • Salimo 136:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yamikani amene anagawa pakati Nyanja Yofiira:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Yesaya 63:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 amene anawawolotsa pamadzi amphamvu moti sanapunthwe, mofanana ndi hatchi m’chipululu?+

  • 1 Akorinto 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale, kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena