Ekisodo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+ Ekisodo 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndilola Aiguputo kuumitsa mitima yawo,+ kuti atsatire Aisiraeli panyanjapo, kutinso ndipezerepo ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magulu ake onse ankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+ Aroma 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ponena za Farao, Lemba linati: “Ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.”+
16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+
17 Koma ine ndilola Aiguputo kuumitsa mitima yawo,+ kuti atsatire Aisiraeli panyanjapo, kutinso ndipezerepo ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magulu ake onse ankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+
17 Pakuti ponena za Farao, Lemba linati: “Ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.”+