Ekisodo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+ Yoswa 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene ndinali kutulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pang’ono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira+ ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira. Aroma 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ponena za Farao, Lemba linati: “Ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.”+
16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+
6 Pamene ndinali kutulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pang’ono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira+ ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira.
17 Pakuti ponena za Farao, Lemba linati: “Ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.”+