Yoswa 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Analandanso dera lochokera kuphiri la Halaki+ lomwe lili moyang’anizana ndi Seiri+ mpaka kukafika ku Baala-gadi,+ kuchigwa cha Lebanoni m’munsi mwa phiri la Herimoni.+ Yoswa anagwira mafumu awo onse ndi kuwapha.+
17 Analandanso dera lochokera kuphiri la Halaki+ lomwe lili moyang’anizana ndi Seiri+ mpaka kukafika ku Baala-gadi,+ kuchigwa cha Lebanoni m’munsi mwa phiri la Herimoni.+ Yoswa anagwira mafumu awo onse ndi kuwapha.+