Deuteronomo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+ Salimo 136:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amenenso anapha mafumu olemekezeka:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+
18 Amenenso anapha mafumu olemekezeka:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+