Numeri 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zinthuzo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa gulu lonse la anthuwo.+
27 Zinthuzo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa gulu lonse la anthuwo.+