Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma musadye+ nyama pamodzi ndi magazi+ ake, amene ndiwo moyo+ wake.

  • Levitiko 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’”

  • Levitiko 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.

  • Deuteronomo 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma musadye magazi ake.+ Muziwathira panthaka ngati madzi.+

  • Ezekieli 33:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Choncho auze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mumadya nyama limodzi ndi magazi ake,+ mumayang’anitsitsa mafano anu onyansa+ ndipo mumakhetsa magazi.+ Kodi pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?+

  • Machitidwe 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena