Yesaya 66:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+ Mateyu 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+
16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+
41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+