Esitere 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ana aamuna 10+ a Hamani+ mwana wa Hamedata amene anali kudana ndi Ayuda.+ Ayuda anapha amuna amenewa koma sanafunkhe+ zinthu zawo. Hoseya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Efuraimu ndamuona akuoneka ngati Turo atabzalidwa pamalo odyetserapo ziweto a msipu wobiriwira.+ Koma iye adzapititsa ana ake kokaphedwa.”+
10 ana aamuna 10+ a Hamani+ mwana wa Hamedata amene anali kudana ndi Ayuda.+ Ayuda anapha amuna amenewa koma sanafunkhe+ zinthu zawo.
13 Efuraimu ndamuona akuoneka ngati Turo atabzalidwa pamalo odyetserapo ziweto a msipu wobiriwira.+ Koma iye adzapititsa ana ake kokaphedwa.”+