Ezekieli 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo.+ Uuze mfumuyo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘“Ndiwe chitsanzo changwiro. Uli ndi nzeru zochuluka+ ndipo ndiwe wokongola kwambiri.+
12 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo.+ Uuze mfumuyo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘“Ndiwe chitsanzo changwiro. Uli ndi nzeru zochuluka+ ndipo ndiwe wokongola kwambiri.+