Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero okondedwanu, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse+ ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi kapena mzimu,+ kwinaku tikukwaniritsa kukhala oyera poopa Mulungu.+

  • 2 Akorinto 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye.

  • Aefeso 5:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+

  • 2 Petulo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chotero okondedwa, pakuti mukuyembekezera zinthu zimenezi, chitani chilichonse chotheka kuti iye adzakupezeni opanda banga,+ opanda chilema ndiponso muli mu mtendere.+

  • Chivumbulutso 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Awa ndiwo amene sanadziipitse ndi akazi,+ ndipo ali ngati anamwali.+ Amenewa ndiwo amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene akupita.+ Iwowa anagulidwa+ kuchokera mwa anthu, monga zipatso zoyambirira+ zoperekedwa kwa Mulungu ndi kwa Mwanawankhosa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena