Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba,+ osasunthika, okhala ndi zochita zambiri nthawi zonse mu ntchito ya Ambuye,+ podziwa kuti zonse zimene mukuchita mu ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+

  • 2 Akorinto 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu.

  • Afilipi 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chitani zimenezi kuti muzitsimikizira kuti zinthu zofunika kwambiri ndi ziti,+ kuti mukhale opanda cholakwa+ ndi osakhumudwitsa+ ena kufikira tsiku la Khristu.

  • 1 Atesalonika 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Achite zimenezi mpaka atalimbitsa mitima yanu ndi kukupangitsani kukhala opanda cholakwa+ ndi oyera pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwa Ambuye wathu Yesu, limodzi ndi oyera ake onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena