Aefeso 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+ Akolose 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tikulengeza,+ kuchenjeza, ndi kuphunzitsa munthu aliyense za ameneyu mu nzeru zonse,+ kuti tipereke munthu aliyense kwa Mulungu ali wokhwima mwauzimu+ mogwirizana ndi Khristu.
27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+
28 Tikulengeza,+ kuchenjeza, ndi kuphunzitsa munthu aliyense za ameneyu mu nzeru zonse,+ kuti tipereke munthu aliyense kwa Mulungu ali wokhwima mwauzimu+ mogwirizana ndi Khristu.