Maliko 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo Yesu anawayankha kuti: “Pamene mkwati ali limodzi ndi anzake, anzake a mkwatiwo sangasale kudya,+ si choncho kodi? Chotero chifukwa chakuti mkwati ali nawo limodzi, sangasale kudya.+
19 Ndipo Yesu anawayankha kuti: “Pamene mkwati ali limodzi ndi anzake, anzake a mkwatiwo sangasale kudya,+ si choncho kodi? Chotero chifukwa chakuti mkwati ali nawo limodzi, sangasale kudya.+