2 “Panopa ndili mʼtulo koma mtima wanga uli maso.+
Ndikumva wachikondi wanga akugogoda.”
“Nditsegulire iwe mchemwali wanga, wokondedwa wanga,
Njiwa yanga, iwe wopanda chilema.
Chifukwa mutu wanga wanyowa ndi mame,
Tsitsi langa lopotanapotana, lanyowa ndi chinyezi cha usiku.”+