Nyimbo ya Solomo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Pabedi panga usiku, ndinaganizira za munthu amene mtima wanga umam’konda.+ Ndinalakalaka kumuona koma iye panalibe.
3 “Pabedi panga usiku, ndinaganizira za munthu amene mtima wanga umam’konda.+ Ndinalakalaka kumuona koma iye panalibe.