1 Samueli 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anali kukonda Davide, ndipo anthu anauza Sauli zimenezi. Sauli atamva nkhani imeneyi anasangalala. Nyimbo ya Solomo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe amene mtima wanga umakukonda,+ tandiuza kumene umakadyetsera ziweto,+ kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu ya namalira pakati pa magulu a ziweto za anzako?”
20 Tsopano Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anali kukonda Davide, ndipo anthu anauza Sauli zimenezi. Sauli atamva nkhani imeneyi anasangalala.
7 “Iwe amene mtima wanga umakukonda,+ tandiuza kumene umakadyetsera ziweto,+ kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu ya namalira pakati pa magulu a ziweto za anzako?”