1 Mafumu 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Bati-seba anagwada n’kuweramira pansi+ pamaso pa mfumu. Mfumuyo inati: “Ukufuna kupempha chiyani?”+ Afilipi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anachita zimenezi kuti m’dzina la Yesu, onse akumwamba, apadziko lapansi, ndi apansi pa nthaka apinde mawondo awo.+
16 Bati-seba anagwada n’kuweramira pansi+ pamaso pa mfumu. Mfumuyo inati: “Ukufuna kupempha chiyani?”+
10 Anachita zimenezi kuti m’dzina la Yesu, onse akumwamba, apadziko lapansi, ndi apansi pa nthaka apinde mawondo awo.+