-
1 Mafumu 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno Bati-seba anati: “Pali kanthu kakang’ono kamodzi kamene ndikufuna kupempha. Musandikanire pempho langa.” Mfumuyo inamuuza kuti: “Pemphani mayi anga, sindikukanirani.”
-