Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+ Yohane 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndine m’busa wabwino, nkhosa zanga ndimazidziwa,+ izonso zimandidziwa,+ Aheberi 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,
11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+
20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,