Yesaya 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+
23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+