1 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu Solomo inakonda akazi ambiri achilendo+ kuphatikiza pa mwana wamkazi wa Farao.+ Inakonda akazi achimowabu,+ achiamoni,+ achiedomu,+ achisidoni,+ ndi achihiti.+
11 Mfumu Solomo inakonda akazi ambiri achilendo+ kuphatikiza pa mwana wamkazi wa Farao.+ Inakonda akazi achimowabu,+ achiamoni,+ achiedomu,+ achisidoni,+ ndi achihiti.+