Genesis 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+ Rute 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso ndikugula Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira+ libwerere pacholowa chake, kutinso lisafafanizike pakati pa abale ake ndi mumzinda wathu. Inu ndinu mboni+ lero.”
37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+
10 Komanso ndikugula Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira+ libwerere pacholowa chake, kutinso lisafafanizike pakati pa abale ake ndi mumzinda wathu. Inu ndinu mboni+ lero.”