Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+
7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+