Genesis 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Potsirizira pake, masiku oti Rabeka abereke anakwana, ndipo m’mimba mwake munali mapasa.+ Genesis 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mbiri ya Esau, kapena kuti Edomu,+ ili motere: Numeri 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsiku lina Mose anatumiza amithenga kuchokera ku Kadesi kumene iwo anali, kupita kwa mfumu ya Edomu,+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene ationekera ife.+ Obadiya 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+
14 Tsiku lina Mose anatumiza amithenga kuchokera ku Kadesi kumene iwo anali, kupita kwa mfumu ya Edomu,+ kukanena kuti: “Abale anu Aisiraeli+ akuti, ‘Inu mukudziwa bwino za mavuto onse amene ationekera ife.+
10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+