Genesis 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+ Deuteronomo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+ Ezekieli 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti Edomu walanga nyumba ya Yuda ndipo akupitiriza kuilanga ndi kuichitira zinthu zoipa kwambiri,+ Aroma 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Ndinakonda Yakobo, koma Esau ndinadana naye.”+
30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+
7 “Usaipidwe ndi Mwedomu, chifukwa ndi m’bale wako.+ “Usaipidwe ndi Mwiguputo, chifukwa unali mlendo m’dziko lawo.+
12 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti Edomu walanga nyumba ya Yuda ndipo akupitiriza kuilanga ndi kuichitira zinthu zoipa kwambiri,+