Malaki 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Esau+ ndinadana naye. Pamapeto pake, mapiri ake ndinawasandutsa bwinja.+ Malo ake okhala, ine ndinawasandutsa malo okhala mimbulu ya m’chipululu.”+ Aheberi 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muonetsetsenso kuti pasakhale wadama kapena aliyense wosayamikira zinthu zopatulika, ngati Esau,+ amene anapereka udindo wake monga woyamba kubadwa pousinthanitsa ndi chakudya chodya kamodzi kokha.+
3 “Esau+ ndinadana naye. Pamapeto pake, mapiri ake ndinawasandutsa bwinja.+ Malo ake okhala, ine ndinawasandutsa malo okhala mimbulu ya m’chipululu.”+
16 Muonetsetsenso kuti pasakhale wadama kapena aliyense wosayamikira zinthu zopatulika, ngati Esau,+ amene anapereka udindo wake monga woyamba kubadwa pousinthanitsa ndi chakudya chodya kamodzi kokha.+