Yeremiya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ine ndalumbira pa dzina langa+ kuti Bozira+ adzakhala chinthu chodabwitsa, chotonzedwa ndiponso malo owonongedwa.+ Iye adzakhala wotembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.
13 “Ine ndalumbira pa dzina langa+ kuti Bozira+ adzakhala chinthu chodabwitsa, chotonzedwa ndiponso malo owonongedwa.+ Iye adzakhala wotembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.