4 “Popeza kuti Edomu akunena kuti, ‘Ife tawonongedwa, koma tibwerera ndi kukamanga malo athu owonongedwawo,’ Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Iwo akamanga, koma ine ndikagwetsa.+ Anthu adzatcha malo awowo, “dera la zoipa” ndipo iwowo adzatchedwa, “anthu okanidwa ndi Yehova+ mpaka kalekale.”