Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 137:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+

      Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+

  • Yesaya 34:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Pakuti lupanga langa+ lidzakhala magazi okhaokha kumwambako. Lupangalo lidzatsikira pa Edomu+ ndi pa anthu amene ndikufuna kuwawononga+ mogwirizana ndi chilungamo changa.

  • Obadiya 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nyumba ya Yakobo idzakhala ngati moto,+ nyumba ya Yosefe idzakhala ngati malawi a moto ndipo nyumba ya Esau idzakhala ngati mapesi.+ Motowo udzayatsa mapesiwo ndi kuwanyeketsa. Sipadzakhala wopulumuka aliyense wa nyumba ya Esau,+ pakuti Yehova mwiniyo wanena.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena