Obadiya 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+ Obadiya 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Iwe sunayenera kumangoonerera mosangalala pa tsiku limene m’bale wako anakumana ndi tsoka.+ Sunayenera kusangalala pa tsiku limene ana a Yuda anali kuwonongedwa.+ Sunayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene iwo anamva zowawa. Mika 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Tsopano mitundu yambiri ya anthu idzasonkhana kuti ikuukire. Mitunduyo ikunena kuti, ‘Tiyeni timuwononge ndipo maso athu aone kuwonongeka kwa Ziyoni.’+
10 Chifukwa chakuti m’bale wako Yakobo unam’chitira zachiwawa,+ manyazi adzakugwira.+ Iwe udzawonongedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.*+
12 “Iwe sunayenera kumangoonerera mosangalala pa tsiku limene m’bale wako anakumana ndi tsoka.+ Sunayenera kusangalala pa tsiku limene ana a Yuda anali kuwonongedwa.+ Sunayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene iwo anamva zowawa.
11 “Tsopano mitundu yambiri ya anthu idzasonkhana kuti ikuukire. Mitunduyo ikunena kuti, ‘Tiyeni timuwononge ndipo maso athu aone kuwonongeka kwa Ziyoni.’+