Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 49:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Monga mmene Sodomu ndi Gomora pamodzi ndi midzi yapafupi inawonongedwera,+ Edomu adzawonongedwanso moti palibe munthu amene adzakhalanso m’dzikolo. Mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo,”+ watero Yehova.

  • Ezekieli 35:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti unali kusangalala chifukwa chakuti cholowa cha nyumba ya Isiraeli chinawonongedwa, ine ndidzachitanso chimodzimodzi kwa iwe.+ Iwe dera lamapiri la Seiri ndiponso Edomu yense, mudzasanduka bwinja,+ ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”+

  • Obadiya 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iwe Temani,+ anthu ako amphamvu adzachita mantha,+ chifukwa chakuti aliyense wa iwo adzaphedwa+ ndi kuchotsedwa m’dera lamapiri la Esau.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena