Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iye anawononga mizindayi, ngakhale Chigawo chonsecho ndi anthu onse a m’mizindayi, kuphatikizapo zomera za panthaka.+

  • Deuteronomo 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Adzanena mawuwo akadzaonanso sulufule, mchere+ ndi kutentha,+ moti m’dzikomo simungabzalidwe mbewu, simungaphuke kalikonse ndipo simungamere chomera chilichonse, mofanana ndi Sodomu ndi Gomora,+ Adima+ ndi Zeboyimu,+ mizinda imene Yehova anaiwononga mu ukali ndi mkwiyo wake.+

  • Yeremiya 50:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 “Monga mmene Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora+ pamodzi ndi midzi yake yapafupi,+ dzikolo lidzawonongedwanso moti palibe munthu amene adzakhalanso mmenemo. Mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo,”+ watero Yehova.

  • Amosi 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “‘Ndinabweretsa chiwonongeko pakati pa anthu inu chofanana ndi chimene Mulungu anabweretsa pa Sodomu ndi Gomora.+ Pamenepo inu munakhala ngati chitsa cholanditsidwa pamoto+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.

  • Zefaniya 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,+ Mowabu adzakhala ndendende ngati Sodomu,+ ndipo ana a Amoni+ adzakhala ngati Gomora, malo odzaza zomera zoyabwa ndiponso mchere ndiponso malo abwinja mpaka kalekale.*+ Otsala mwa anthu anga adzafunkha zinthu zawo, ndipo otsala a mtundu wa anthu anga adzawagwira ukapolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena