Genesis 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mafumuwa anachita nkhondo ndi mafumu otsatirawa: Bera mfumu ya ku Sodomu,+ Birisa mfumu ya ku Gomora,+ Sinabi mfumu ya ku Adima,+ Semebere mfumu ya ku Zeboyimu,+ ndi mfumu ya ku Bela (kapena kuti ku Zowari).+ Hoseya 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi ndikusiyirenji iwe Efuraimu?+ Kodi ndikuperekerenji kwa adani iwe Isiraeli?+ Kodi ndikusandutsirenji ngati Adima?+ Kodi ndikuchitirenji zofanana ndi zimene ndinachitira Zeboyimu?+ Mtima wanga wasintha+ ndipo pa nthawi imodzimodziyo wadzaza ndi chisoni.
2 mafumuwa anachita nkhondo ndi mafumu otsatirawa: Bera mfumu ya ku Sodomu,+ Birisa mfumu ya ku Gomora,+ Sinabi mfumu ya ku Adima,+ Semebere mfumu ya ku Zeboyimu,+ ndi mfumu ya ku Bela (kapena kuti ku Zowari).+
8 “Kodi ndikusiyirenji iwe Efuraimu?+ Kodi ndikuperekerenji kwa adani iwe Isiraeli?+ Kodi ndikusandutsirenji ngati Adima?+ Kodi ndikuchitirenji zofanana ndi zimene ndinachitira Zeboyimu?+ Mtima wanga wasintha+ ndipo pa nthawi imodzimodziyo wadzaza ndi chisoni.