Yeremiya 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu ameneyo akhale ngati mizinda imene Yehova waigonjetsa popanda kuimvera chisoni.+ M’mawa kwambiri azimva kulira kofuula ndipo masana azimva chizindikiro chochenjeza.+ Amosi 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Ndinabweretsa chiwonongeko pakati pa anthu inu chofanana ndi chimene Mulungu anabweretsa pa Sodomu ndi Gomora.+ Pamenepo inu munakhala ngati chitsa cholanditsidwa pamoto+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.
16 Munthu ameneyo akhale ngati mizinda imene Yehova waigonjetsa popanda kuimvera chisoni.+ M’mawa kwambiri azimva kulira kofuula ndipo masana azimva chizindikiro chochenjeza.+
11 “‘Ndinabweretsa chiwonongeko pakati pa anthu inu chofanana ndi chimene Mulungu anabweretsa pa Sodomu ndi Gomora.+ Pamenepo inu munakhala ngati chitsa cholanditsidwa pamoto+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.