Oweruza 9:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndiyeno Abimeleki anamenyana ndi mzindawo tsiku lonse, n’kuulanda. Anapha anthu amene anali mumzindawo+ ndipo anaugwetsa+ n’kuthira mchere panthaka ya mzindawo.+ Salimo 107:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lamchere,+Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo. Yeremiya 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhala ngati mtengo umene uli pawokhawokha m’chipululu ndipo zabwino zikadzafika sadzatha kuziona.+ Iye adzakhala m’malo ouma a m’chipululu m’dziko la nthaka yamchere, kumene sikukhala anthu.+
45 Ndiyeno Abimeleki anamenyana ndi mzindawo tsiku lonse, n’kuulanda. Anapha anthu amene anali mumzindawo+ ndipo anaugwetsa+ n’kuthira mchere panthaka ya mzindawo.+
6 Adzakhala ngati mtengo umene uli pawokhawokha m’chipululu ndipo zabwino zikadzafika sadzatha kuziona.+ Iye adzakhala m’malo ouma a m’chipululu m’dziko la nthaka yamchere, kumene sikukhala anthu.+