Yeremiya 50:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Mofanana ndi mmene Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora+ komanso midzi imene anali nayo pafupi,+ ndi mmenenso zidzakhalire ndi Babulo. Palibe aliyense amene adzakhalenso mumzindawo,”+ akutero Yehova.
40 “Mofanana ndi mmene Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora+ komanso midzi imene anali nayo pafupi,+ ndi mmenenso zidzakhalire ndi Babulo. Palibe aliyense amene adzakhalenso mumzindawo,”+ akutero Yehova.