Yesaya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+ Yeremiya 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Monga mmene Sodomu ndi Gomora pamodzi ndi midzi yapafupi inawonongedwera,+ Edomu adzawonongedwanso moti palibe munthu amene adzakhalanso m’dzikolo. Mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo,”+ watero Yehova. Yeremiya 51:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Anthu sadzatenga mwala kuchokera kwa iwe kuti ukakhale mwala wapakona kapena mwala wapamaziko+ chifukwa udzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.
9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+
18 Monga mmene Sodomu ndi Gomora pamodzi ndi midzi yapafupi inawonongedwera,+ Edomu adzawonongedwanso moti palibe munthu amene adzakhalanso m’dzikolo. Mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo,”+ watero Yehova.
26 “Anthu sadzatenga mwala kuchokera kwa iwe kuti ukakhale mwala wapakona kapena mwala wapamaziko+ chifukwa udzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.