Yeremiya 50:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Monga mmene Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora+ pamodzi ndi midzi yake yapafupi,+ dzikolo lidzawonongedwanso moti palibe munthu amene adzakhalanso mmenemo. Mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo,”+ watero Yehova. Chivumbulutso 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu+ n’kuuponya m’nyanja,+ ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+
40 “Monga mmene Mulungu anawonongera Sodomu ndi Gomora+ pamodzi ndi midzi yake yapafupi,+ dzikolo lidzawonongedwanso moti palibe munthu amene adzakhalanso mmenemo. Mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo,”+ watero Yehova.
21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu+ n’kuuponya m’nyanja,+ ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+