Yesaya 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usana ndi usiku, motowo sudzazima. Utsi wake uzidzakwera m’mwamba mpaka kalekale.+ Dzikolo lidzakhala louma ku mibadwomibadwo.+ Mpaka muyaya palibe amene adzadutseko.+ Yeremiya 49:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Hazori+ adzakhala malo obisalamo mimbulu+ ndipo adzakhala bwinja mpaka kalekale. Palibe munthu amene adzakhala kumeneko, moti mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo.”+
10 Usana ndi usiku, motowo sudzazima. Utsi wake uzidzakwera m’mwamba mpaka kalekale.+ Dzikolo lidzakhala louma ku mibadwomibadwo.+ Mpaka muyaya palibe amene adzadutseko.+
33 “Hazori+ adzakhala malo obisalamo mimbulu+ ndipo adzakhala bwinja mpaka kalekale. Palibe munthu amene adzakhala kumeneko, moti mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo.”+