Ezekieli 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mofanana ndi mmene unasangalalira cholowa cha nyumba ya Isiraeli chitawonongedwa, ine ndidzachitanso chimodzimodzi kwa iwe.+ Iwe dera lamapiri la Seiri, kutanthauza Edomu yense,+ udzasanduka bwinja, ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
15 Mofanana ndi mmene unasangalalira cholowa cha nyumba ya Isiraeli chitawonongedwa, ine ndidzachitanso chimodzimodzi kwa iwe.+ Iwe dera lamapiri la Seiri, kutanthauza Edomu yense,+ udzasanduka bwinja, ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”