Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 137:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+

      Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+

  • Yeremiya 49:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ponena za Edomu, Yehova wa makamu wanena kuti: “Kodi nzeru+ zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zavunda?+

  • Yeremiya 49:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Taonani! Wina adzakwera kenako n’kutsika ngati chiwombankhanga chimene chikufuna kugwira chakudya chake.+ Adzatambasulira mapiko ake pa Bozira,+ ndipo pa tsikulo mtima wa amuna amphamvu a ku Edomu udzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena