Yobu 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iyetu amagwetsa zinthu kuti zisamangidwe,+Zimene iye watseka, palibe munthu amene angazitsegule.+ Salimo 127:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+
127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+