Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 31:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iyenso ndi wanzeru+ ndipo adzabweretsa tsoka.+ Sadzabweza mawu ake+ ndipo adzaukira nyumba ya anthu ochita zoipa.+ Adzalepheretsa anthu amene amachita zopweteka anzawo, kupeza chithandizo chimene amafuna.+

  • Yeremiya 51:64
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire osatulukanso chifukwa cha masoka amene ndikumugwetsera.+ Ndipo Ababulowo adzadzitopetsa okha.’”+

      Mawu a Yeremiya athera pamenepa.

  • Malaki 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Popeza kuti Edomu akunena kuti, ‘Ife tawonongedwa, koma tibwerera ndi kukamanga malo athu owonongedwawo,’ Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Iwo akamanga, koma ine ndikagwetsa.+ Anthu adzatcha malo awowo, “dera la zoipa” ndipo iwowo adzatchedwa, “anthu okanidwa ndi Yehova+ mpaka kalekale.”*

  • Yuda 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komanso mizinda ya Sodomu ndi Gomora ndi mizinda yozungulira mizinda imeneyi,+ inalandira chilango cha moto wosatha,+ motero yaikidwa monga chitsanzo chotichenjeza.+ Anthu ake anachita mofanana ndi amene tatchula aja, pochita dama loipitsitsa ndiponso pogonana m’njira imene si yachibadwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena