Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+ Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+ Yeremiya 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Yehova wanena kuti: ‘Tsopano chizindikiro cha zimenezi kwa inu ndi ichi,+ ine ndikulangani m’dziko lino kuti mudziwe kuti mawu anga adzakwaniritsidwadi moti ndidzakugwetserani tsoka.+
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+
29 “Yehova wanena kuti: ‘Tsopano chizindikiro cha zimenezi kwa inu ndi ichi,+ ine ndikulangani m’dziko lino kuti mudziwe kuti mawu anga adzakwaniritsidwadi moti ndidzakugwetserani tsoka.+