Yeremiya 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Imwani, muledzere, musanze ndi kugwa osadzukanso+ chifukwa cha lupanga limene ndikukutumizirani pakati panu.”’+
27 “Ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Imwani, muledzere, musanze ndi kugwa osadzukanso+ chifukwa cha lupanga limene ndikukutumizirani pakati panu.”’+