Yesaya 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinapondaponda mitundu ya anthu mu mkwiyo wanga, ndipo ndinawaledzeretsa ndi ukali wanga.+ Ndinachititsa kuti magazi awo atuluke mwamphamvu n’kutayikira pansi.”+ Maliro 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kondwa ndipo usangalale,+ iwe mwana wamkazi wa Edomu,+ amene ukukhala m’dziko la Uzi.+Iwenso kapuyo ikupeza.+ Udzaledzera ndipo anthu adzakuona uli maliseche.+ Habakuku 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwenso adzakumwetsa+ ndipo udzaonekera kuti ndiwe wosadulidwa.+ Udzakhuta zinthu zamanyazi m’malo mwa ulemerero.+ Chikho chochokera m’dzanja lamanja la Yehova chidzakupeza+ ndipo ulemerero wako udzasanduka manyazi.
6 Ndinapondaponda mitundu ya anthu mu mkwiyo wanga, ndipo ndinawaledzeretsa ndi ukali wanga.+ Ndinachititsa kuti magazi awo atuluke mwamphamvu n’kutayikira pansi.”+
21 Kondwa ndipo usangalale,+ iwe mwana wamkazi wa Edomu,+ amene ukukhala m’dziko la Uzi.+Iwenso kapuyo ikupeza.+ Udzaledzera ndipo anthu adzakuona uli maliseche.+
16 Iwenso adzakumwetsa+ ndipo udzaonekera kuti ndiwe wosadulidwa.+ Udzakhuta zinthu zamanyazi m’malo mwa ulemerero.+ Chikho chochokera m’dzanja lamanja la Yehova chidzakupeza+ ndipo ulemerero wako udzasanduka manyazi.