Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+ Obadiya 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Iwe sunayenera kumangoonerera mosangalala pa tsiku limene m’bale wako anakumana ndi tsoka.+ Sunayenera kusangalala pa tsiku limene ana a Yuda anali kuwonongedwa.+ Sunayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene iwo anamva zowawa.
7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+
12 “Iwe sunayenera kumangoonerera mosangalala pa tsiku limene m’bale wako anakumana ndi tsoka.+ Sunayenera kusangalala pa tsiku limene ana a Yuda anali kuwonongedwa.+ Sunayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene iwo anamva zowawa.